LyricFind Logo
LyricFind Logo
Profile image icon
Lyric cover art

Lemmi be yo man

Apple Music logo
Deezer logo
Spotify logo
Lyrics
Chikondi changa ndi chozama
Pa iwe sichonama
Jus be my girl
Eh eh
Jus be my girl
Lemmi be yo man

Tambala akaona msoti
Ndipo akafilanso zoti
Ka chick ko kali hot
Amakathamangitsa
Mpakana akagwire
Kaya kathawire pa minga
Kaya kathawire patchire
Samaonetsa kutopa
Jacob atafunitsitsa Rachael
Anapatsidwa zaka 7
Zoti agwire ntchito
Atamaliza zaka 7
Anapatsidwa zina 7
Poti anafunitsitsa
Sanaotse kutopa

Baby baby ndakuuza ndikufuna eh
Koma iwe taona Ungodumphadumpha eh
Koma ngakhale undikane
Koma ngakhale unditukwane
Ine sindifooka
Sindionetsa kugonja

Chikondi changa ndichozama
Pa iwe sichonama
Jus be my girl
Ndizakukonda kwa muyaya
Chikondi changa ndi chakuya
Jus be my girl
Lemmi be yo man

Ngati umafuna ndi chikondi
Ndiye usakaike
Ngati ukufuna ndi chikondi
Nde usadikire
Kuchokera unyamata
Kukafika ukalamba
Ndizakukonda the same
Osaonetsa kutopa
Ibwere mvula ndizakhala yako umbrella
Kungadzidzire ndizakusunga pa chifuwa
Pangatalike chikondi changa sichizasintha
Sichizasintha sichizaonetsa kutopa

Oh baby baby
Usamandiyankhe zamatama eh
Tikakumana bwanji umangofuna za drama eh
Sinditopa kubwera kwanu
Kaya uzandilumitsa galu
Sindionetsa kuopa
Sindionetsa kugonja

Chikondi changa ndi chozama
Pa iwe sichonama
Jus be my girl
Ndzakukonda kwa muyaya
Chikondi changa ndi chakuya
Jus be my girl
Lemmi be yo man

Eh
Jus be my girl
Lemmi be yo man
Den am gonna be yo lover
Jus be my Hava
Am gonna be yo Adam
Take my hand baby Lets dance
Encious bring the beat

Chikondi changa ndi chozama

Chikondi changa ndi chozama
Pa iwe sichonama
Jus be my girl
Ndizakukonda kwa muyaya
Chikondi changa ndi chakuya
Jus be my girl
Lemmi be yo man

WRITERS

Arthur Mailos

PUBLISHERS

Lyrics © O/B/O DistroKid

Share icon and text

Share


See A Problem With Something?

Lyrics

Other

LyricIQ Analysis

Top Emotion

Enjoyment

Sentiment
Thumbsup IconThumbsup Icon
Theme

Substance Use