LyricFind Logo
LyricFind Logo
Profile image icon
Lyric cover art

Ndende

Apple Music logo
Deezer logo
Spotify logo
Lyrics
Chonona chifuma kudzira abale
Mmela mpoyamba mbewu ndi pa nursery
Kuongola mtengo
Ndi pomwe uli waung'ono
Ukangokula Ndi kukhwima
Sizingatheke
Chikondi si mpikisano
Mtima wanu mmalo
Khalani Ndi nthawi yodziwana kaye

Osati kukumana chinkhoswe mawa,
Ukwati nkucha
Kungofera ndapata ka chiphadzuwa,
Kapena khumutcha
Mtendere wa mumtima
Upambana zonse
Please take one step at a time

Take your time
Osapupuluma
Kusankha wachikondi molakwika
Imeneyo Ndi Ndende
Osangotinso Ndende
Koma Ndende ya moyo onse

Chikondi chisamangodzetsa pressure
Misonzi daily kumangokhetsa
Ngati sizikuyenda
Bwanji kungozileka
Osakakamira
Fupa lokakamiza
Limatswa mphika

Miyoyo yambiri yapululuka
M'dzina la chikondi
Ma suicide cases ochulukanso
Nkhani zake za chikondi

Mtendere wa mumtima
Upambana zonse
Please take one step at a time

Take your time
Osapupuluma
Kusankha wachikondi molakwika
Imeneyo Ndi Ndende
Osangotinso Ndende
Koma Ndende ya moyo onse

WRITERS

Arthur Smile

PUBLISHERS

Lyrics © O/B/O DistroKid

Share icon and text

Share


See A Problem With Something?

Lyrics

Other

LyricIQ Analysis

Top Emotion

Sadness

Sentiment
Thumbsup Icon
Theme

Abuse and Violence