LyricFind Logo
LyricFind Logo
Profile image icon
Lyric cover art

Sekelerani Mama

Apple Music logo
Deezer logo
Spotify logo
Lyrics
Hallo mamaaa haa

Mammi tabwerani
Mwana wanu ndili ndi nkhani
Ndikufuna ntakuuzani
Choyamba ndithokoze
Za chikondi chanu
Chikondi chosatsimbika
Kuchokera ndili mwana
Kuzafika ndili apa
Chinsinsi cha moyo wanga onse ndi chikondi chanu

Ndikadwala inu osagona
Ndikalira inu munkalira
Panopano ndikufuna mukusekelera

Sekelerani Mama
Nyadirani Amama
Today is a beautiful day
Sekelerani Mama
Nyadirani Amama
Am singing this song for you
Am happily dancing for you for you
Today is a wonderful day

Nthawi zina ndine gwelo
Lakukhumudwa kwanu Amama pepani
Nthawi zina ndine kasupe
Wa misonzi yanu Amama pepani
Ntchito zanga zanyasi
Zakhala zokupepusani
Malo osiyanasiyana omwe mumapita
Ndakupepusani ku mpingo
Pamaso pa achibale
Mothandizidwa ndi Mbuye
Nyasi zonse ndazisiyaa

Sekelerani Mama
Nyadirani Amama
Today is a beautiful day
Sekelerani Mama
Nyadirani Amama
Today is a beautiful day
Am singing this song for you
Am happily dancing for you
Today is a wonderful day

Mama mama mama mama mwalira
Nthawi yaitali chifukwa cha ine
Koma koma panopa
Nyadirani mwana wanu watsopano
Mwana wanu watsopanoo

Sekelerani Mama
Nyadirani Amama
Today is a beautiful day
Sekelerani Mama
Nyadirani Amama
Today is a beautiful day
Am singing this song for you
Am happily dancing for you
Today is a wonderful day

WRITERS

Arthur Mailos

PUBLISHERS

Lyrics © O/B/O DistroKid

Share icon and text

Share


See A Problem With Something?

Lyrics

Other

LyricIQ Analysis

Top Emotion

Enjoyment

Sentiment
Thumbsup IconThumbsup IconThumbsup Icon
Theme

Sexual