Ndina lota ndita blowa Ndita mveka my song in every corner
Ndina wona maso mphenya ndita beba my face on every poster
Ndina lota zosatheka, zitatheka mavuto ata chepa
Ndina gwada Na pemphera Namalenga Ndu dziwa ama mvela
Zitafika povuta ndi na sweka
Zitafika potentha ndi ma ngolila
Mtima ku sweka misonzi Ku ukha
Moyo ukakuvuta osasiya Ku Pusha
Thokoza chauta, tsiku lizadza,
Thokoza chauta, tsiku lizadza