Please drop me location to your heart I'm tryna slide
I've been in the sky for way too long I'm tryna land
Drop you that location you can pull up to my side
Pull up to Malawi usachedwe sunga nthawi
Undi patse mapu aku mtima kwako
Undi patseko ka love kaku mtima kwako
Undi patse mapu aku mtima kwako
Undi patseko ka love kaku mtima kwako
Ndimaganizila ndima lota tikuyenda limodzi
Ku jambulisa ma photo tiku seka limodzi
Undi patseko chikondi, usandipweteke chonchi,
Usandi lembetse m'madzi, usandigwetse Misonzi,
Chikondi chako ndi Chipata
Olo ma exsi Sindimawahala
Please drop me location to your heart I'm tryna slide
I've been in the sky for way too long I'm tryna land
Drop you that location you can pull up to my side
Pull up to Malawi usachedwe sunga nthawi
Undi patse mapu aku mtima kwako
Undi patseko ka love kaku mtima kwako
Tizapita kwa makolo ana adzakhala folo
Undi patse mapu aku mtima kwako
Undi patseko ka love kaku mtima kwako
Tizapita kwa makolo ana adzakhala folo
Undi yankhe lelo zamawa ayi
Ndiku tengele kwathu ku Malawi
Nzaku patsa mimba I swear Wallahi
So i wanna love you yakwana yokha nthawi
Usiku kuchedwa kucha funa ntakuwona
Iwe wekha uuhuh nditha ku bona uuuhuh
Nkaku wedzela ka nsomba uuhuh
Undi patse mapu aku mtima kwako
Undi patseko ka love kaku mtima kwako
Tizapita kwa makolo ana adzakhala folo
Undi patse mapu aku mtima kwako
Undi patseko ka love kaku mtima kwako
Tizapita kwa makolo ana adzakhala folo