Koma nde mwatchena, abwana mwatchena koma nde mwachena adona mwatchena
Koma nde mwatchena, abwana mwatchena koma nde mwachena adona mwatchena
Kuvara ngat asokela momo mwinatso telala alimomo
Kuvara ngat asokela momo mwinatso telala alimomo
Kuvara kwanjiku kuvara kwanjiku?
Kutchena kwanjiku Kutchena kwanjiku
Kutchena tizitchena koma nauyu watiposa tosefe watiposa
Taonani, Taonani, Taonani, Taonani, Taonani, Taonani
Kuvara kwanjiku kuvara kwanjiku?
Kutchena kwanjiku Kutchena kwanjiku
Kuvara tizivara koma nauyu watiposa tosefe watiposa